Kishore Kumar Hits

Sangie - Confusion текст песни

Исполнитель: Sangie

альбом: Confusion


Sangie ya know
Hello, it's me
I was wondering if I could talk to you for a minute
Hello, it's me
I won't take much of your time
Ndiye ndingonena mumve
Amuna aja Mbuye, zolenga zanu kunoko
Zandisautsa, zandiyimitsa head yeah, confusion
Umva waagwililira, am'gwililira ah-ah
Am'gwililira ndipo am'chita nkhanza
Nkhani zonyasa zokhazokha
Ndiye mundithandize ineyo
Ndingapange zosakomera inuyo
Mundilimbitse ineyo
Ndisaganize zochimwira inuyo
Muwathandize iwowa
Asapange zosakomera inuyo
Ndipo mutilimbitse ifeyo
Tisaganize zochimwira inuyo
I don't wanna fight no man no
I don't wanna go again solo
Sindufuna kuti ndipange zinthu zina, poti ndakwiya ine
Sakumaona iwo
Ndi ana omwe eti
Sakumaona inu
Olo ali m'bale eeh
N'chiwanda chanji ichichi chawagwira awawa
N'chiwanda chanji ichichi chawalipira heh-eh
Am'gwililira, wagwiliridwa (ah-ah-ah)
Am'gwililira ndipo am'chita nkhanza
Nkhani zonyasa heh-eh
Ndiye mundithandize ineyo
Ndingapange zosakomera inuyo
Mundilimbitse ineyo
Ndisaganize zochimwira inuyo
Muwathandize iwowa
Asapange zosakomera inuyo
Ndipo mutilimbitse ifeyo
Tisaganize zochimwira inuyo
Oh-oh-oh...
Oh-oh-oh...
Yeah
Hmm
Ndiye mundithandize ineyo
Ndingapange zosakomera inuyo
Mundilimbitse ineyo
Ndisaganize zochimwira inuyo
Muwathandize iwowa
Asapange zosakomera inuyo
Ndipo mutilimbitse ifeyo
Tisaganize zochimwira inuyo
Ndiye mundithandize ineyo
Ndingapange zosakomera inuyo
Mundilimbitse ineyo
Ndisaganize zochimwira inuyo
Muwathandize iwowa
Asapange zosakomera inuyo
Ndipo mutilimbitse ifeyo
Tisaganize zochimwira inuyo (yeahhh)

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Eti

2023 · сингл

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель