Kishore Kumar Hits

Sangie - KOKA INA текст песни

Исполнитель: Sangie

альбом: KOKA INA


Baby
Love ya bwanji iyi
Ndikamakhala pena
Osamvetsetsai
How do we connect
How do we make sense
How did we meet
Ih yeah ih yeah
Anthu awiri from different worlds
Koma zochita kuchita limodzi
Anthu ochoka different worlds
Mtima kugunda kugunda pamodzi
Chikondi ichi ichi
Sindimachimvetsabe eti
Love iyi iyi
Sindimayimvetsabe eti
Love iyiyi
Chikondi ichichi
Love iyiyi
Chikondi ichichi
You know seh gangster
Ndayesetsa kukhala stable
Kudzigwira komabe I'm not able
Eti ine kuthawawa
Kubisabisa
Kuzembazemba
Osafuna kuonetsera
Kuti ndazelezeka nawe baby
Wandimalizitsamo eti
Yey yey mmm yeah
You're like kokaina
You get me higher inna
Love Love yeah
Chikondi ichi ichi
Sindimachimvetsabe eti
Love iyi iyi
Sindimayimvetsabe eti
Love iyiyi
Chikondi ichichi
Love iyiyi
Chikondi ichichi
Pena we do think we don't deserve love mmm
Everybody needs love (Needs love)
Everybody deserves to be loved
(Deserves to be loved)
He my kokaina
He gets me higher inna
In love love yeah
Chikondi ichi ichi
Sindimachimvetsabe eti (No no no)
Love iyi iyi
Sindimayimvetsabe eti (No no no)
Love iyiyi
Chikondi ichichi
Love iyiyi
Chikondi ichichi
This love
This love yeah
Love iyiyi
Chikondi ichichi (Chikondi ichichi)
Love iyiyi (This love yeah)
Chikondi ichichi
Mmmm

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Eti

2023 · сингл

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель