Aaah eeeh ooh
(Nefia ndima feel de fiya)
Finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Ah finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Samakondwa mkamamwetulira
Mumtima amafuna nditagwa
Kumbali amangondijeda
Pamaso kumati ndi anzanga
Vuto likangoti lagwa
Limadziwa dziko lonse
Samafuna nditapata
Samakondwa nane Kose
Ey chineke Godo
Mwayiputayi ndi nkhondo
Ey Mulungu wanga
Mwandionetsa adani onse
Ndisapezeko wa banja
Angokhalira ma damage
Ndisakwezedwe kuntchito
Ati ndine wa maknhwala
Oh oh aah no
My God can never let me down
Mmh ngwabwino
Amandikonda nthawi zonse
Finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Ah finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani ndi kundikondetsa abale
Kudela lawo news kumbali
Ena pamaso ngati amandikonda koma kumbaliko
Ndi Lucifer angakhale
Siza ndale kwangali hurry hurry sangandinyanyale
Nnaneso n'nanale
Ndimvinire Mulungu wanga
Yeah ndikwezere buluku langa
(Feel defiya)
Sizokhwefulira, izi zimafuna kunyindilira
Koma ndati ah hah
Eh eh ah ndi a iwe
Ndingowona committee yonse ikumwetulira
Maria Magadalena kuvina ndi angelo ena
Koma ziwongole ziwongole pamakwelero
Mama de nazatsara
Finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Ah finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Ah finally, Mbuye inu finally
Finally, Mbuye inu finally
Mwandionetsa abale pa mavuto
Mbuye inu finally
Mwandidziwitsa adani anga onse
Mbuye inu finally
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя