Ndapilira ine Ndapilira ineyo Ndapilira ine Mmmh baby Tsiku lokha lija lakwana Lolumbira paguwa lija lakwana (inde) Mayi ako akusangalala Bambo ako nthungululu aku lulutira (iwe) Wawachotsa manyazi Achitaponya stepe opanda nthumazi (eeh eeh) Uyu ndi mkazi opilira Muziphinjo amandichengetera (ine) Sangafane ndi enawa Pakagwa vuto amayamba kuthawa (eeeh) Uyu ndiodziwa mwambo Analangidwa ku nsondo Azinzanga akukonda Azibale akukonda Iwe khala phee Me I belong to you Baby bany I'll die for you Ndapilira nthawi yaitali Kuti ifeyo tikhale limodzi Taona zambiri zowawa Mmoyowu sitingasimbe It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh) It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh) Bwenzi Langa lero ndi tsiku lamayankho Auziletu azizanko Kuti nzeru zako zinathera paine Palibeso wina koma unakonda ine zozembelana zija zatha Moti iwe ndi ine ndi banja (yey yay) Yatsa candle light Kusonyeza tsogolo lathu liri so bright (eh eh) Ansanje akakolope mnyanja Iwe ndine tayanjana (yey yay) Ndiwe Mayi wa ana anga Ndiwe Bambo wa fuko langa (yey yay) Umandimvetsa kukoma Umandimvetsa ma sugar (iwe iwe) Iwe ndine mpakampaka Day yobwera yesu Ndapilira nthawi yaitali Kuti ifeyo tikhale limodzi Taona zambiri zowawa Mmoyowu sitingasimbe It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh) It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh) Ndapilira nthawi yaitali Kuti ifeyo tikhale limodzi Taona zambiri zowawa Mmoyowu sitingasimbe It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh) It's our happy day (umh umh) It's your wedding day (umh umh)