Mwana wanga
Ngati umandikonda, mvetsela
Mwana wanga
Ngati umaukonda moyo wako sintha
Mwana wanga
Ngati umandikonda, mvetsela
Mwana wanga
Ngati umaukonda moyo wako sintha
Ndati palibe, palibe, palibe
Angakugwile dzanja, pamavuto
Ndati palibe, palibe, palibe
Angakugwile dzanja, pamavuto mwanawe
Uuuuh Mwana wanga mvetsela, mvetsela
Uuuuh Mwana wanga mvetsela, mvetsela
Komabe njoya, mosamala poti nkhondo ndi anansi
Amabwela ngati achibale, koma mpeni atapanila kuphanzi
Komabe njoya, mosamala poti nkhondo ndi anansi,
Amabwela ngati achibale, koma mpeni atapanila kuphanzi
Uuuuh Mwana wanga mvetsela, Mvetsela
Uuuuh Mwana wanga mvetsela, mvetsela
Komabe njoya, mosamala poti nkhondo ndi anansi
Amabwela ngati achibale, koma mpeni atapanila kuphanzi
Komabe njoya, mosamala poti nkhondo ndi anansi,
Amabwela ngati achibale, koma mpeni atapanila kuphanzi
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя