Makonda ena nakonda madhutu makonda ena oyera ngati mzungu makonda Lemme point were ma choices ndakonda iweyo babe you ma Valentino ×7 Makonda makonda galu anakonda fupa, Nanga ine nakonda super, stake anakonda kupha You're my valentino nkazi oneka bwino ah Don't cheat end you know tationse pa low Anthu salephera zokambakamba hun kufuna Kusokoneza plan kumakunamiza zikhani akuti siwe MG 1 Uyike zima headset usamamve zawo uzingomva Zagazokha akayamba kuthoka trash ali ku zala iwe uzingochoka Makonda ena nakonda madhutu makonda ena oyera ngati mzungu makonda Lemme point were ma choices ndakonda iweyo babe you ma Valentino ×7 Zokonda kusiyana zokonda zanthu sizingakhare zawo Ndibelekere ana zabanja lanthu iwo alibe gawo alipo ka gulu Wo hater koma izo ndi zawo alipo ka mulu wo jeda akamanenya bawo Ati ndakwatira dhutu kunyoza ngati simunthu Zokonda zanthu ndi zanthu chikondi ndi 2 2 2 Uyike zima headset usamamve zawo uzingomva Zangazokha akayamba kuthoka trash ali ku zala iwe uzingochoka Makonda ena nakonda madhutu makonda ena oyera ngati mzungu makonda Lemme point were ma choices ndakonda iweyo babe you ma Valentino ×7 Pali ka nkhani tabwerani mami talowani mami tikambirane Pali ka nkhani tabwerani mami talowani mami tikambirane Makonda ena nakonda madhutu makonda ena oyera ngati mzungu makonda Lemme point were ma choices ndakonda iweyo babe you ma Valentino ×7