Kishore Kumar Hits

MartseMw - Woloka текст песни

Исполнитель: MartseMw

альбом: Martse Singles


Martse, (ndawoloka)
Too ghetto too gutter, (ndawoloka)
Yeah we still keeping fresh man
Minga inandibaya
Thought i'd never walk again
Koma chisomo cha Jah Jah
Told me boy don't lose again
Koma look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka
Just look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka
Yeah usanalakwe utha kupatsidwa fail yeah
Usanalakwe utha kugona mu cell yeah
Your true friends mkuzakupanga bail yeah
Your fake friends will have stories to tell yeah
Igwa kawiri dzuka katatu
Osasaka mbiri osasaka anthu
Kuwona zikhomo ndiye kukula kwathu
Koma kugonjetsedwako simbali yathu
Moyo utha kuvuta ndizotheka
Munthu mkubalalika ndizomveka
Anzako kukutsika, ukupenya
Koma tsiku ndi lomodzi nawe udzayenda, (fresh man)
Minga inandibaya
Thought i'd never walk again
Koma chisomo cha Jah Jah
Told me boy don't lose again
Koma look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka
Just look at me now ndawoloka, (yeah)
Popanda njira paja ndawoloka,(yeah uh)
Kuyipitsiridwa mbiri daily daily
Kukhomemeledwa ku ntchito ku daily daily
Ena kupatsidwa ma promotion
Koma iwe uli stuck pompaja daily daily
Kusukulu ku ndiye ma sup mbwee
Anzako kudutsa pompo iwe ma repeat mbwee
Kumafika pena paja pongo loser faith
Koma wachoka kutalipanopa sungaleke eh
Moyo utha kuvuta ndizotheka
Munthu mkubalalika ndizomveka
Anzako kukutsika, ukupenya
Koma tsiku ndi lomodzi nawe udzayenda, (fresh man)
Minga inandibaya
Thought i'd never walk again
Koma chisomo cha Jah Jah
Told me boy don't lose again
Koma look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka
Just look at me now ndawoloka, (yeah)
Popanda njira paja ndawoloka,(uh uh)
Huh, ukachimwitsa usanalowe m'banja
Anthu amachulukitsa zokamba
Mudzamudyetsa chani mwana?
Kodi Mulungu anamaliza kugawa?
Ena ati muchotse ena musunge
Koma utaya bwanji mphatso ya Ambuye
Koma be strong as you fight through the pain and i tell you
God will always make a way ey
Moyo utha kuvuta ndizotheka
Munthu mkubalalika ndizomveka
Anzako kukutsika, ukupenya
Koma tsiku ndi lomodzi nawe udzayenda, (fresh man)
Minga inandibaya
Thought i'd never walk again
Koma chisomo cha Jah Jah
Told me boy don't lose again
Koma look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka
Just look at me now ndawoloka
Popanda njira paja ndawoloka

Popanda njira paja ndawoloka
Ndawoloka
Ndawoloka
Ndawoloka

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители