Lero Nde tigona panjatu Spice up ngati rajah Akaziwa amatiwazatu Mukununkhila Ndi mkatimo Mukununkhila ndi mkatimo Ndamva kwayatsidwa ganja Ndamva kununkhila mkatimo Ndabwera kudzaona nyanja Koma mvuuu zili mkatimo Ichi nde Ndi chi type changa Ndichigoba ndichitchulila salimo Musanditayitse time yanga man Mukununkhila Ndi mkatimo Nkhanga zanunkhiza ka dollar kanga kutumiza Mukumachenjela mukachifukiza (ehem) Ndisachite kukutupitsa Mu ka hustle bagmo kukupisa Ka donah kako kuphumitsa Kukuteaser, kukuliza Kukumenya nde kungokutchukitsa Yakungana ya ma fazala Khutu ngati chigoneleni chadzana Ndabwera tokha ma guy sizomakana Kukonda ngini izi zokha sindimakana Change for what am in okay now Kukometsa pa Malo Zabwino sanena My action men with a silencer