Kishore Kumar Hits

Maskal - Wampeza текст песни

Исполнитель: Maskal

альбом: Umunthu


Ngati umafuna munthu oseka naye
Wokhala naye, wocheza naye
Lero wamupeza
Umafuna munthu woposa nzako
Womuwuza nkhani, zoposa nkhani
Lero wamupeza
Umafuna womupatsa chikondi chako
Nyengo ingasinthe bwanji
Iwe ndi wako
Umafuna womupatsa mtima wako
Anganyoze bwanji, ndi wako
Dziwa baby, wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, lero wamupeza
Wokhala naye baby, wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, lero wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Wakhala nthawi yayitali bwanji uli chotere?
Undiuze ndidziwe baby
Ndilore ndiyeseko mwayi wanga undivomele
Ndidziwe baby
Misozi yako ndipuputa
Nkhawa zako ndifufuta
Mantha ako ndifufuta ineyo
Misozi yako ndipuputa
Nkhawa zako ndifufuta
Mantha ako ndifufuta Ine
Dziwa baby, wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, lero wamupeza
Wokhala naye baby, wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, lero wamupeza
Wamupeza baby, oh wamupeza (ooh oooh)
Wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Nkhawa zako ay yah yah
Mantha ako ay yah yah
Misonzi yako ay yah ndipuputa Ine
Nkhawa zako ay yah yah
Mantha ako ay yah yah
Misonzi yako ay yah ndipuputa Ine!
Dziwa baby, wamupeza
Wotsitsa mtima wako baby, lero wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, wamupeza
Wokhala naye baby, lero wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza (ooh)
Wamupeza (wamupeza), oh wamupeza
Wamupeza wamupeza, oh wamupeza (eya yah)
Wamupeza, oh wamupeza
Wokhala naye baby, wamupeza
Wosunga chikondi chako baby, lero wamupeza
Woseka naye baby, wamupeza
Wamupeza, lero wamupeza
Wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza wamupeza, oh wamupeza
Wamupeza wamupeza, oh wamupeza

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители