Ndaenda ntunda wautali
Kusaka kufuna namwali
Ndifuna ndikhazikike ineeee
Ndatopa kukonda olakwika
Onena kumati okanikaaaa
Ndifuna ndi khazikike ineeeoo
Lelo ndifuna kukondedwa
Ndatopa ndikunyozedwa aaa
Chikondi chonse tenga ndakupasa babiee
Zili ndiwe kuti uzandi thaweeee
Zili ndiwe kuti uzandi kondeee
Zili ndi iwe kuti uzandi zunzeeee
Poti chikondi chonse ndapeka
Kwa iwe
Undilole ndikhale wapantima wako
Ndizolowele ndikhale mmoyo mwako
Ndikhazikike ndiweee
Ngakhale andinene ndine olephela
Mu dzikolako ndikhale olemelaaa
Ndikhazikike ndiweeeee
Ndatopa ndikunyozedwaaa
Lelo ndifuna kukondedwaaaa
Chikondi chonse tenga ndakupasa
Babeeee
Zili ndiwe kuti uzandi thaweeee
Zili ndiwe kuti uzandi kondeee
Zili ndi iwe kuti uzandi zunzeeee
Poti chikondi chonse ndapeka
Kwa iwe
Kuti uzandithaweee
Uzandi kondeeee
Uzandi zinzeeee
Zili ndi iwe
Kuti uzandikondeee
Uzandi thaweee
Uzandi zunzeeee
Zili ndi iweeee
(Ndi iwe... yooooo)
Zili ndiwe babeeee
Tidzaseka
Ndidzalileee
Ndidzakodwaaa
Haaaa
Ndiwe
Ndi iwe
Ndiwe
Ndidzasekaaa
Ndidzakodwaaa
Ndidzalileeeee babeeee
Zili ndi iwe babieee
Ndiwe babeee... uuu
Ndiwe babeeeeeee
End
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя