Yeah yeah, yah, yah, yah
Yeah, yah, yah, yah
Umamva bwanji baby?
Ukakhala ndi Ine baby
Nthumazi imandigwira baby
Nthawi zonse ukatalikira
Ndimagwidwa ndi maganizo
Ndimasowa chithandizo
Ndidziwa bwanji za mtima wako
Poti udziwa wekha
Ukakhala ndi anzako (awo)
Umawawuza chani za ine (awo)
Pali zambiri ndimafuna nditadziwa
Tandiuze
Umamva bwanji baby?
Umaganiza chani baby?
Umamva bwanji baby?
Ndiwuze ndidziwe
Umamva bwanji baby?
Umaganiza chani baby?
Umamva bwanji baby?
Ndiwuze ndidziwe
Ndidziwe yah aah
Ndiuze ndidziwe!
Mu mtima mwako ndi Ine
Kodi ndimakukwanira?
Ukakhala kumbali kodi umandinyadira?
Popeza unandidziwa
Utapatsidwanso mwayi wosankha
Ungasankhe ine!
Ndiwuze ndidziwe
Nkutheka sizili bwino (inde)
Ine mkumati zili bwino (inde)
Pali zambiri ndimafuna nditadziwa!
Tandiuze
Umamva bwanji baby?
Umaganiza chani baby?
Umamva bwanji baby?
Ndiwuze ndidziwe
Umamva bwanji baby?
Umaganiza chani baby?
Umamva bwanji baby?
Ndiwuze ndidziwe!
Ndiwuze ndidziwe!
Ndidziwe, ndiwuze ndidziwe
Umamva bwanji baby? (heee)
Umaganiza chani baby? (heeeeeee)
Umamva bwanji baby? (heee)
Ndiwuze ndidziwe (ukakhala kutali)
Umamva bwanji baby? (ndimakhala ndi nkhawa)
Umaganiza chani baby? (ndimakhala ndi ntchito)
Umamva bwanji baby? (ndiuze ndidziwe)
Ndiwuze ndidziwe!
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя