Kishore Kumar Hits

Macelba - Chisankho текст песни

Исполнитель: Macelba

альбом: Chisankho


Unawina mtima wanga ndiwe boma
Chikondi chakwela nde sitingatsutse boma
Inu nde a chair
Kulamulira boma
Mamie muimanso silingaluze boma
Mamie
Muli ndi mtima wachikondi
Olo ndilakwitse muli ndi mtima wachisoni
Makutu m'natseka muli ndi mtima wachigonthi
Siinu a njilu mulibe mtima wachizondi
Ndinene tchutchutchu
Olo atsine khutu
Sindimva za munthu
Kapena ndi juju
Mtima wanga za inu unachongelatu
Ndabwera ndabwera apapa ndafikiratu
Mamie iwee ndasankha
No regret
Mamie iwee ndasankha
There is no recount
Oh wina
Basi no wina
Palibeso wina
Ndiwe Owina
Oh wina
Basi no wina
Palibenso wina
Ndiwe owina eee eeeh

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители