Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Chinambalala текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: How Long?


Anambalala atengetsana mama
Ife kwathu ndikuwonera
Kulakwilana, kuba ayamba kuwulura mama
Limbikani muyaluke
Dyera la chuma mukhadzulana abale
Ife sitikuleletsani
Munali limodzi mwezi watha omwewu
Lero zinthu zatembenuka
Ife tukungodabwa kutuluka chothawa
Nasonkhanitsa anthu kuwauza bodza
Chipanichi mchanga siya mchipani choyipa
Kudzaganizira anthu mudziona liti
Inu abale anga tidzadzuka liti?
Chilichonse chibwere tingonthamangira
Amakoma mantha kudzapempha vote
Akalowa m'boma ife atiyiwala
Amalawi ndife opusitsa mama
Sitidziwa chomwe tifuna
Abale Angwazi amkangowanamiza choncho
Mwana wathu alibe vuto
Lero Agama mwakakamiza choncho
Muchotse nduna zako nzakuba
Mukachotsa nduna adzapanga chipani chawo
Inu nomwe muchisapota
Chilichonse tikuyika ndale amama
Mchaka zinthu sizikuyenda
Mudzi umodzi mafumu awiri achani?
Kwinakutu ndi kuzisaka
Lija ndikale mudayamba ndale adadi
Kapumeni tipitilize
Mwakula bwana musalekele pomwepo
Muchotsebe nduna zakuba
Ife tukungodabwa kutuluka chothawa
Nasonkhanitsa anthu kuwauza bodza
Chipanichi mchanga siya mchipani choyipa
Kudzaganizira anthu mudziona liti
Inu abale anga tidzadzuka liti?
Chilichonse chibwere tingonthamangira
Amakoma mantha kudzapempha vote
Akalowa m'boma ife atiyiwala

Ife tukungodabwa kutuluka chothawa
Nasonkhanitsa anthu kuwauza bodza
Chipanichi mchanga siya mchipani choyipa
Kudzaganizira anthu mudziona liti
Inu abale anga tidzadzuka liti?
Chilichonse chibwere tingonthamangira
Amakoma mantha kudzapempha ife
Akalowa m'boma ife atiyiwala
Ife tukungodabwa kutuluka chothawa
Nasonkhanitsa anthu kuwauza bodza
Chipanichi mchanga siya ntchito ayi ndichoyipa
Kudzaganizira anthu mudziona liti
Inu abale anga tidzadzuka liti?
Chilichonse chibwere tingonthamangira
Amakoma mantha kudzapempha vote
Akalowa m'boma ife atiyiwala
Eeh eeh eeh eeh
Eeh eeh eeh eeh
Ife tukungodabwa kutuluka chothawa
Nasonkhanitsa anthu kuwauza bodza
Chipanichi mchanga siya mchipani choyipa
Kudzaganizira anthu mudziona liti
Inu abale anga tidzadzuka liti?

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель