Yo man ting a beatiful girl you know Mr Lucius Banda and Sergio man once again Highway productions man Heheha Kodi Tina ali konko? Aah iye a likonko? Mumuyitane ali konko Aah iye a likonko? (eh wabwera) Iwe Tina tabwera Ndili ndi timawu Ndikupita ku Lilongwe Ndikafune ntchito Undipatse chala Tina Ndivekeko mphete Kuti ikhale chikole cha chikondi changa Ena amanena banja si ndalama Koma ine nditi lero Banja siumphawiso Ndukafuna ndalama, tidzamange banja Usazavutike Tina ndi umphawi wanga Ndiwe okongola Ndiwe okongola Tina Ndiwe okongola undidikilire Ndiwe okongola Ndiwe okongola weche weche Ndiwe okongola, undidikilire Wakusalala, wakusalala Tina Wakusalala, undidikilire Wakusalala, perfume wapokopoko Wakusalala undidikilire Ndikuziwa kuti kwanu sunkadya therere Tina ndiyesesa chonde kuti uzakondwe Ndizakuchotsa ku Mangochi kunka Kumangoni Uzasiya kudya nsomba uzizadya nyama Akabwera amuna ozakufunsira Uwaonetse mphete yanga Uli pachibwenzi Zina zimakhala nkhakamira za ma benz awo Tina Udzikanitsitse mama Zikhwaya zammangochi Ndiwe okongola Ndiwe okongola Tina Ndiwe okongola undidikilire Ndiwe okongola Perfume weche weche Ndiwe okongola, undidikilire Wakusalala, wakusalala Tina Wakusalala, undidikilire Wakusalala, wakusalala weche weche Wakusalala undidikilire Kodi tina ulikumva iwe? Ooh ulikumva? Pomwe ndinena ulikumva iwe? Aiye ulikumva? Amuna ambiri lero ndi aulesi zedi Angolowa m'banja alibe kalikonse Mkazi akamamphe nyama Ati okonda chuma Usampute mwana waeni ulibe kalikonse Pali akazi ena Ndi wonyada udyo Ndalama zandiwo mai Kuthera kuziphoda Kukongola kwa mkazi zikope ndizizi Ndikugwira ntchito Tina ndikusekelera Ndiwe okongola Ndiwe okongola Tina Ndiwe okongola, undidikilire Ndiwe okongola Perfume wapokopoko Ndiwe okongola, undidikilire Wakusalala, wakusalala Tina Wakusalala undidikilire Wakusalala, wakusalala wecheweche Wakusalala, undidikilire Iwetu Tina palibetu wina koma ndiwe wekha Wawu wakusalala kwenjidyi kwangali Wane ndi wawe mwina ndolite ey Iwetu Tina palibetu wina koma ndiwe wekha Wawu wakusalala kwenjidyi kwangali Wane ndi wawe mwina ndolite ey Once upon a time In the year 2-G Lucius Banda says you man They must fit a far shine me know Wind up your body and check your body girl He's had a load out, you can't complain Your face is so bright, your face is so shine Like a moon in the sky, sine into the good things you know Wind up your body and check your body girl He's had a load out, you can't complain Ndiwe okongola Ndiwe okongola Tina Ndiwe okongola undidikilire Ndiwe okongola, perfume wa wecheweche Ndiwe okongola undidikilire Wakusalala, wakusalala Tina Wakusalala undidikilire Wakusalala, wakusalala wecheweche Wakusalala undidikilire Atopitopi ali konko Ayi yeah ali konko Alikonde ali konko Ay yeah ali konko A Boniface muli konko inu? Ooh oh ali konko (A Banda muli konko?) (Ay yeah muli konko)