Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Tikamalira текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: Life


Kodi ndi angati akukondwa?
Kodi ndi angati akulira?
Cheteyutu ndi mantha
M'mitima muli zinkhani
Nzeru zayekha adanyika
Abale muti amava za anzanu?
Olo tinyozeke bwanji
Nafe Malawi ndi kwathu
Muja adayimbila Galatiya
Tayamba bwino kumaliza mwachithaya
Mudali bwenzi lathu ambiri
Agalu okuwakuwa tidali ochepa
Mwa luso lanu mudatimanga pa chain
Agalu tonse tidakhala chete
Pomwe kumacha panyumba paja pabedwa
Ufulu ndi chuma tangotsala ndi ufa

Abale munthu samayipa zonse
Pali zambiri zofunika mapanga
Tikuyamika zitukuko zambiri
Zimene mwayesetsa kutipangira
Mwamanga zambiri makamaka misewu
Mwathetsa njala ndipo anthu tawona
Koma abwana chikuvuta ndichani?
Zoyipa zayamba kufufuta zabwino
Kodi ndi angati akukondwa?
Kodi ndi angati akulira?
Cheteyutu ndi mantha
Mu mtima muli zinkhani
Nzeru zayekha adanyika
Abale muti amava za anzanu?
Olo tinyozeke bwanji ife
Nafe Malawi ndi kwathu
Tikamalira mudzitimvera
Timati inu m'bambo athu
Tikayimba musamakwiye
Timafuna mumve malango
Tikamalira mudzitimvera
Timati inu m'bambo athu
Tikayimba musamabane
Mudzingomvapo langizolo
Ay yeah yeah yeah yeah
Ay yah yah yah yah
Ay yeah yeah yeah yeah
Mayo mayo
Mmh
Wobeleka sake ndathu ena
Poti wobwezela ufikire kwa ana
Abale mmafika pothamangitsa kazembe
Zotsatila zidzaphinja aphawi
Muli ndi zonse zosowa mkapa moyo
Olo nzungu atakwiya mungathe kulimba
Koma ifeyo amphawi akumudzi
Timadalira thandizo la azunguwo
Kumvetsa chisoni anzathu alimi
Alima mbewu kusowa ogula
Ogula fodya munawathamangitsa
Koma zonsezi ovutika ndi ife
Mitengo yafodya ya masiku ano
Zomvetsa chisoni mlimi ali m'mavuto
Wa business ngokondwela popereka
Ma okala atilanda m'ma china
Kodi ndi angati akukondwa?
Kodi ndi angati akulira?
Cheteyutu ndi mantha
M'mitima muli zinkhani
Nzeru zayekha adanyika
Abale muti amava za anzanu?
Olo tinyozeke bwanji ife
Nafe Malawi ndi kwathu
Tikamalira mudzitimvera
Timati inu m'bambo athu
Tikayimba musamabane
Timafuna mumve malango
Tikamalira mudzitimvera
Timati inu m'bambo athu
Tikamayimba musamatide
Timangofuna muchite chilondola
Ay yeah yeah yeah yeah
Ay yah ooh
Oooh
Tililiti-titete-titili-tete
Hahaha
Ay yah yah
Kodi ndi angati akukondwa?
Kodi ndi angati akulira?
Cheteyutu ndi mantha
Mu mitima muli zinkhani
Nzeru zayekha adanyika
Abale muti amava za anzanu?
Olo tinyozeke bwanji
Nafe Malawi ndi kwathu
Tikamalira mudzitimvera
Timati inu m'bambo athu
Tikayimba musamakwiye
Timafuna mumve malango
(Tikamalira mudzitimvera)

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель