Let us remember to be grateful to God For keeping us alive Akapitao nkhanza Ana sankanena kanthu Ana sanali woyipa Mumkangotseka ndinu Anali adokotala oyesetsa kusamala mbumba Adafa mbiri yachabe Wolakwa Akapitao Let us also not forget that God Chisoni Agadama Chikweza pumanayeni Agogo amkamukonda Koma Kapitao zimkamunyasa Momwe adathera athu Agogo asakudziwa Amkamva zotha itha Kapitao amkapha anthu Ngati ankazunza anthu ali nduna uyo Kodi adzazunza bwanji akafikapo? Amkakondera akwawo ali wamba uyo Kodi ena tidzatani akafikapo? Milandu yonse amkawina olo alakwe uyo Kodi adzawina bwanji akalowa m'boma? Akwathu nthenda yathu ndi kuyiwala inu Komatu m'makumbuka tinavutika Do not forget that God the almighty father Has given us many other blessings In the course of the past years Ali ndi magazi m'manja Yekhayo chonde mtayeni Ndi danger mukugwirayo Mukuyatsa moto wa petulo Tukwana nzimu kumanda Ambiri anatisiya Wosalakwa ali mu shire Adawapha pofuna mpando ♪ Agogo amkayesetsa Kuyambitsa zinthu zabwino Kapitao akazipinda Mkumapangira nkhanza Card linalipo bwino Idali njira yodziwilana Adayamba kutsekela nsika Sukulu ndi chipatala Ngati ankazunza anthu ali nduna uyo Kodi adzazunza bwanji akafikapo? Amkakondera akwawo ali wamba uyo Kodi ena tidzatani akafikapo? Milandu yonse amkawina olo alakwe uyo Kodi adzawina bwanji akalowa m'boma? Akwathu nthenda yathu nkuyiwala inu Komatu m'makumbuka tinavutika ♪ Tithokoze bwana Muluzi Wathetsa nkhanza zonsezi Kukhala kupusa kwathu Kubwenzelaso nkhanza 1964 adalipo mu parliament Lero adakaliso phungu Kodi mudzapuma liti? Amalawi tatopa nanu Muleke tione zina Mulore Bingu alowe Tione za mtundu wina Bingu ndi munthu ofatsa Wopanda mbiri zakupha Maphunziro ndi okwana Tiyeni tione zina Ngati anazunza anthu ali nduna uyo Kodi adzazunza bwanji akafikapo? Amkakondera akwawo ali wamba uyo Kodi ena tidzatani akafikapo? Milandu yonse amkawina olo alakwe uyo Kodi adzawina bwanji akalowa m'boma? Akwathu nthenda yathu ndi kuyiwala inu Komatu m'makumbuka tidavutika Let us also not forget that God the almighty father Has given us many other blessings In the course of the past years Therefore i wish you all my people A very very happy and prosperous new year Ngati anazunza anthu ali nduna uyo Kodi adzazunza bwanji akafikapo? Amkakondera akwawo ali wamba uyo Kodi ena tidzatani akafikapo? Milandu yonse amkawina olo alakwe uyo Kodi adzawina bwanji akalowa m'boma? (Akwathu nthenda yathu ndi kuyiwala inu) (Komatu m'makumbuka tidavutika)