Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Mundikumbuke текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: The Very Best


Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha

Amayi asanafe
Adasiya mawu
Udzafunefune bambo uli nawo
Udzakwere bus upite ku Lilongwe
Poti ndafa mwina adzakutenga
Bambo ako ngopata
Uwafufuze zedi
Kumeneko amawatchula Amasina
Umasiye otere
Mudakali ndi moyo
Umakhalatu umasiye owawa
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Nzanga tayimani
Bambo anga adalimani
Ine wamasiye mudakali ndi moyo
Simungamve chisoni
Ndikuvutika adadi
Mundithandize ndimalize sukulu
Ndine mwana wapatchire
Ndakula ndi mayi
Koma mwina mawa mudzandifunanso
Muli ndi mkazi wina
Wovuta kwambiri
Sindingakhale nanu mundithandize
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha

Mwana wamasiye
Azimayi achiwiri
Muwasamale monga ana anunso
Simungamve chisoni ana akuvutika
Muwasamale monga ana anunso
Amayi asadafe oh adasiya mawu
Udzafunefune bambo uli nawo
Udzakwere bus upite ku Lilongwe
Kumeneko amawatchula Amasina
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha

Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke kumbuke abambo
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha (adadi)
Mundikumbuke mundikumbuke
Mundikumbuke abambo ndatsala ndekha

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель