Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Mayi Zembani текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: Yahwe


Abambo anawasiya amayi ndili wang'ono
Ana asanu ndi awiri amayi okha
Amayi opanda ntchito, osaphunzira
Kuwalanda katundu yense, opanda chifundo
Mudasankha uchidakwa, kusiya wana
Tidasanduka masikini abambo mulipo
Kuvundukula ma bin, kutolatola chakudya
Kupita ku misika, tikatole za magwafa
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Pamene tidali kukula, anatitola azungu
Kutilipilira sukulu, kutigwiritsa maganyu
Tinkakolopa mchimbuzi, opanda nsapato kuphanzi
Kuvutikira sukulu, abambo mukumwa mowa
Adayesetsa amayi, mpaka lero ndakula
Nditangoyamba ine ntchito, amayi kumamwalira
Ukwati wanga amayi, sanawuwone
Mwana ndi nkazi wanga, amayi anawazemba ooh!
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Ndithokoza kwa Ambuye, kamba kankazi wanga
Andisamala mwachikondi, ngati mayi wanga
Mundandilanda amayi, mwandipatsa Roller
Abambo anachoka, mwandipatsa Jonny ooh
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Chabwino mayi Zembani
Mupume mumtendere
Kumwamba muli amayi
Mukonze malo anga
Mama we love you
This song is specially dedicated to you mom
It's been three years since you lay down there
But we will still remember you
Your are a hero mama
You are a hero mama

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель