Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Ndimasilira текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: Enemy


Khalani khala oh, osangalala
Zosowa zanga Mbuye mumandipatsa
Koma chimodzi chomwe chimandivuta oh
Ndimawasowa mayi wanga
Ndimakhumbira mayi wanga
Mkajomba kumunda mayi
Kundimana nsima
Mkathawa sukulu mayi kundikwapula
Ndimkangoti nkhanza mayi
Ine chibwana aa aa!
Chinali chikondi mama inu
Ndimakhumbira mayi wanga
Lero ndikulira (mayi wa weh)
Amayi wanga
Analowa mmanda asanadyelele
Anzathu alinawo mayi wo timawasilira
Akamawapatsa chitenje
Timasilira mama ine
Chauta kumwamba oh mundisamalire
Amayi ndi mayi aposa zonse
Inu muli nawo amoyo muwasamalire
Timasilira mama ife
Timasilira mama ife

Ndikamakumbuka oh zophika zawo
Kholowa, bonongwe mama maka chisoso
Akati achape mama ngati wamira mayi
Ndimawasowa mayi wanga
Ndimakhumbira mayi wanga
Tisamanamizane anzanga kuti umasiye
Ndi umphawi okha, usiwa kapena njala
Ungapeze zonse chuma banja mkutchuka
Udzawasowa mayi wako
Ndimasilira mayi ine
Lero ndikulira (mayi wa weh)
Amayi wanga
Analowa mmanda asanadyelele
Anzathu alinawo mayi wo timawasilira
Akamawapatsa chitenje
Timasilira mama ine
Chauta kumwamba oh mundisamalire
Amayi ndi mayi aposa zonse
Inu muli nawo amoyo muwasamalire
Timasilira mama ife
Timasilira mama ife

Lero ndikulira (mayi wa weh)
Amayi wanga
Analowa mmanda asanadyelele
Anzathu alinawo mayi wo timawasilira
Akamawapatsa chitenje
Timasilira mama ine
Chauta kumwamba oh mundisamalire
Amayi ndi mayi aposa zonse
Inu muli nawo amoyo muwasamalire
Timasilira mama ife (masiku onse mama)
Timasilira mama ife (helele oh mother's day)
Achikhala ali moyo (timasilira mama ife)
Akanaphika thowa (timasilira mama ife)
Dzidzukulu mkumamwa (timasilira mama ife)
Oh mother's day (timasilira mama ife)
Pa ukwati wanga (timasilira mama ife)
Ooh yah
Ambuye muwapatse anthu akufa
Chiuziro chosatha
Muwalitse nyumba zawo
Awuse ndi mtendere
Awuse mu mtendere
Amen!
Amama amama amama
Amama amama amama
Ooh amawo amawo amawo
Amen!
Amama amama amama
Amama amama amama
Ooh amawo amawo amawo
Ah amawo amawo amawo

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель