Mulibe mtima wachikondi (amayi inu)
Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu)
Ndichiyani mukufuna (amayi inu)
Kuti musangalale (kuti mama inu)
Chikhala wena mukanayamika
Achepelenji amuna a chikondi
Akazi anzanu akulila mama
Muli ndi tsoka losasimbika wawa
Mukanjoyanjoya akazi wanga muzandipeza
Nkhani zomwe ndikumazimva zikundiliza
Ndinakutenga kumudzi uli ofatsa
Unali mkazi wa ulemu kodi watani?
♪
Ine ndayesetsa kuonetsa chikondi changa
Ndinali munthu ovuta ndinasintha ine
Ku m'mawa ndikakusiya kuntchito kwanu
Ndamva kuti ukumachoka ndi amuna ena
Mulibe mtima wachikondi (amayi inu)
Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu)
Ndichiyani mukufuna? (amayi inu)
Kuti musangalale (kodi mama inu)
Chikhala wena mukanayamika
Achepelenji amuna a chikondi
Akazi anzanu akulila mama
Muli ndi tsoka losasimbika wawa
Zimamvetsa inu chisoni masiku ano
Akazi atayilila mokhumudwitsa
Amakudyetsa mankhwala ati upuse
Chilichonse chomwe anene udzingolola
Helele aha
♪
Ati kandisiye ku casino iwe kulola
Akakumana ndi zibwenzi iwe ukugona
Bambo wabwinobwino wazalezeka
Kuthandiza akwawo onse anamuletsa
Adamuletsa
Adamuletsa
Mulibe mtima wachikondi (amayi inu)
Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu)
Ndichiyani mukufuna? (amayi inu)
Kuti musangalale (kodi mama inu)
Chikhala wena mukanayamika
Achepelenji amuna a chikondi
Akazi anzanu akulila mama
Muli ndi tsoka losasimbika wawa
♪
Helele ey hu yeah lemme go again
(Three, two, one)
Mulibe mtima wachikondi (amayi inu)
Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu)
Ndichiyani mukufuna (amayi inu)
Kuti musangalale (kodi mama inu)
Chikhala wena mukanayamika
Achepelenji amuna a chikondi
Akazi anzanu akulila mama
Muli ndi tsoka losasimbika wawa
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя