(Sonye on the beat)
Eh oh oh oh!
Ndamva kulira zinganga
Nthungululu ndi ng'oma pokopoko
Ndawonera anamwali kutchena
Anyamata wonunkhira perfume
Ndamva dj khutchukhutchu
Anyamata, asungwana okonda dance
Akuponya ndalama ponse ponse
Mabotolo a champagne bu bu bu
Thamangani abale mudzaone
Anzathu ndi ukwati woyera
Akuchimuna kukonda castel
Akuchikazi nawo ku challenger
Mkazamupeza nane wachikondi
Kulikonse nzayenda naye
Mkazamupeza nane wachikondi
Kulikonse nzayenda naye
Kuyenda ngati ngumbi
Kuyenda ngati ngumbi, (ooh)
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe, (oh nyada)
Kuyenda ngati ngumbi
Zothothola mapiko
Kuyenda ngati ngumbi
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe
Uyende ngati ngumbi
Zothothola mapiko
♪
Bayibulo limatiwuza
Sibwino anthu wokondana
Kumakhala motalikana
Usapeleke mwayi kwa satana
Muphunzire kudyela pamodzi
Kupita kumunda limodzi
Ku chikwati kupita limodzi
Kukasambaso limodzi
Kuyenda ngati ngumbi
Kuyenda ngati ngumbi, (kuyenda ngati ngumbi)
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe, (oh nyada)
Kuyenda ngati ngumbi
Zothothola mapiko
Kuyenda ngati ngumbi
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe
Uyende ngati ngumbi
Zothothola mapiko
Oh huu!
Oh ooh
Pang'ono, pang'ono
Eh Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono
Uh huh, uh huh, uh huh
Uh huh, uh huh, uh huh
Kuyenda, kuyenda
Kuyenda ngati, kuyenda ngati
Kuyenda ngati nkhunda aah
Kuyenda ngati, kuyenda ngati
Kuyenda ngati nkhunda aah
Kuyenda ngati ngumbi
Kuyenda ngati ngumbi, (kuyenda ngati ngumbi)
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe
Kuyenda ngati ngumbi
Zothothola mapiko
Kuyenda ngati ngumbi
Kulikonse limodzi
Kuyenda ngati nkhunda
Moyo wathu wonse
Chikondi nchosowa
Ukachipeza iwe
Uyende ngati ngumbi
Zothothola mapiko
Oh huu!
Ooh ooh
Pang'ono, pang'ono
Eh pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
Pang'ono, pang'ono, pang'ono
(Pang'ono)
Поcмотреть все песни артиста