Come close baby Feel my heartbeat You're the only one I want to marry This is for you baby Aaah-ha aah-ha Kodi umadziwa kapena ayi? Ndiwe wokongola Kodi m'madzi kapena ndi mkaka umasamba iweyo? Nanga kodi umadya chiyani kuti udziwongoka? Ukandigwira m'manja mwako kufewa Ngati tsaya la khanda Hunnie ndikutsatsa mpaka kwanu Mayi wako mkawaone Mtima wandikanika kupilira Chuma changa udye ndiwe Baby, baby, baby, baby iwe Baby usapenye kwina Udzipenya kuno, (baby iwe) Ine ndili ndi chikondi (baby look this side) Chofuna Iwe baby, (baby, baby ooh ooh) Nena chomwe ukusowa Udzingoloza iwe (we shall buy baby) Mkazi wokongola chonchi (your wish is my command) Ndani sangapenge? Baby usapenye kwina (don't look aside) Udzipenya kuno, (just look at me) Ine ndili ndi chikondi (just look around) Chofuna Iwe baby, (you're my love) Nena chomwe ukusowa Udzingoloza Iwe (you're special) Mkazi wokongola chonchi (your wish is my command) Ndani sangapenge? Whoa, yeah yeah yeah yeah Ha-ha-ha Ndakhala ndikumakusilira mu nthawi yayitali (ha, yeah yeah yeah yeah) Ndiye kumangopita kutali Ngati anditukwana awa (ha-ha-ha) Mtayang'ana kukongola kwako Mkaziyang'ana kunyasa kwanga Koma pansi pamtima ndimkati poza Mamuna sanyasa Koma baby Tandiyang'ana mmaso mwanga Wandibela mtima wanga Ngakhale udzindikana sindigonja Mamie Ine ndakukonda Baby, baby usapenye Baby usapenye kwina (look at me baby) Udzipenya kuno, (just aside) Ine ndili ndi chikondi (count on me baby) Chofuna Iwe baby, (I'm on your-) Nena chomwe ukusowa (look at me baby) Udzingoloza Iwe (your wish is my command) Mkazi wokongola chonchi Ndani sangapenge? (what is it about you?) Baby usapenye kwina Udzipenya kuno Ine ndili ndi chikondi Chofuna Iwe Nena chomwe ukusowa Udzingoloza Iwe Mkazi wokongola chonchi Ndani sangapenge? Baby usapenye kwina Udzipenya kuno Ine ndili ndi chikondi Chofuna Iwe Nena chomwe ukusowa Udzingoloza Iwe (Mkazi wokongola chonchi)