Kishore Kumar Hits

Lucius Banda - Bwerera текст песни

Исполнитель: Lucius Banda

альбом: LOVE & HATE (The 20th and Final Release)


Mmmh mami oh oh oh
Baby oh
Baby come back
Oh ooh whoa
Kodi dzulo timabwela kunja kukada
Kodi komwe muliko
Mukumakwanitsa kudya?
Nanga ukumatha bwanji
Kupita ku ntchito
Ndafuna udziwe, ine sizikuyenda
Kuchokera tsiku lomwe iwe udachoka
Panyumba padasintha
Lero ndine mulendo
Bed kugula ndekha sindikwanitsa
I want you to know
My lucky pends on you
Ndayamba ndi kale
Kuyitana osabwera
Mkazi wanga uliko?
Tandiyankha ine ndidziwe
Kuyang'anira kunjira
Kuti mwina ndingakuone
Mkazi wanga uliko?
Tabwerera unandi-iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe
Ndimkangoti sukachedwa ukabwerera
Poganiza zabwino udasiya kumbuyo
Ndimkangoti ukatuwa kapena kuguga
Udzandigwadira, udzandichondelera
Kodi ndi mwamuna uti wakuyiwalitsa ineyo
Zukumandiwawa ukunjoya kopanda ine
Akumandiuza anzanga anakuona
Ukusangalala, moyo wako wasuntha
Ndayamba ndi kale
Kuyitana osabwera
Mkazi wanga uliko?
Tandiyankha ine ndidziwe
Kuyang'anira kunjira
Kuti mwina ndingakuone
Mkazi wanga uliko?
Tabwerera unandi-iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe
Bwerera, bwerera iwe

Ndayamba ndi kale
Kuyitana osabwera
Mkazi wanga uliko?
Tandiyankha ine ndidziwe
Kuyang'anira kunjira
Kuti mwina ndingakuone
Mkazi wanga uliko?
Tabwerera unandi-iwe
Ndasintha ine, bwerera
Sintha ine, bwerera iwe
Ndalakwa ine, bwerera
Bwerera iwe, bwerera iwe
Bwerera iwe, bwerera iwe
Bwerera iwe, bwerera iwe

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Life

2016 · альбом

Time

2013 · альбом

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Ritaa

Исполнитель