Zambiri yanu ndinamva Akhungu onse osamva Ena wosayenda Kungowakhuza Inu nyengo zawo zinasitha Nane ndifuna mundikhudze Chonde Musandipitilire Ndatsegula manja (mulore zimu wanu mwa ine ukhazikike) Yesu anamva mphamvu zikuchoka Nzimayi winawake atamugwira Mavuto ake onse ndikuchoka Amadwala basi iye ndikuchira Nane Mbuye wanga Mundigunde Mukandiwolotse pa mafunde Ndikudziwa pena ndine khutukumve Koma mukafuna kukandi user mundiyuze Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha Mukandikhuza nyengo zanga Mumachita zazikulu izo ndinamva Simkaika konse I wanna see your glory I wanna testify ukulu wanu ndiwuone Koma sindichokachokachoka Mpaka Mundikhudzekhudzekhudze Koma Sindichokachokachoka Mpaka mundikhudze khudze ine Mbuye wanga chonde mundikhudze Ndikalakwitsa chonde mundiuze Ndikamachepa chonde mundikuze Osalora Satana andizunze Zolakwika zonse muzichotse Inu ndi amene mungakonze Pandekhapa palibe ndingachite Nde chonde mudzindisamalira nthawi zonse Chonde musalore moyo wanga Satana adzaleponso sizanga Chonde musalore Mbuye wanga Satana akolope moyo mwanga Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha Mukandikhudza nyengo zanga Mumachita zazikulu izo ndinamva Simkaika konse I wanna see your glory I wanna testify ukulu wanu ndiwuone Koma Sindichokachokachoka Mpaka mundikhudzekhudzekhudze Koma sindichokachokachoka Mpaka mundikhudze khudze ine Mpaka mundikhuze ine yeah aaw aah Mpaka mundikhuze iye yeah aaw aah Mukandikhudza, nyengo zanga zisitha Mukandikhudza nyengo zanga Mumachita zazikulu izo ndinamva Simkaika konse I wanna see your glory I wanna testify ukulu wanu ndiwuone Koma Sindichokachokachoka Mpaka mundikhudzekhudzekhudze Koma sindichokachokachoka Mpaka mundikhudze khudze ine Mumachita zazikulu izo ndinamva Simkaika konse I wanna see your glory I wanna testify ukulu wanu ndiwuone Koma Sindichokachokachoka Mpaka mundikhudzekhudzekhudze Koma sindichokachokachoka Mpaka mundikhudze khudze ine