Kishore Kumar Hits

Gwamba - Lipenga текст песни

Исполнитель: Gwamba

альбом: Lipenga


Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Lapilatuu
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Nyengo yovuta koma osakhulupilira
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Koma jah jah sazakukhulupilira
Akufa adzauka, Kaya osauka
Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
Tidzaona misonzi
Panzerepo limodzi
Yeah adzati
Mfana ndakupatsa Zima chance
Lero nde palibe zama story
Mulungu nde salandira Benz
Palibe zoti kuseri ukamukhole
Kaya uli ndi ma doller or rands
Tsiku lomaliza lokha iwe sorry
Palibe zoti Kaya unali ndima fans
Panzere udzakhalapo wekha usaitole
Nde bwanj umachimwabe mulungu ndiwabwno koma osamuyesa
Ngati ufuna kululumuka ukaona tchimo kumaziletsa
Kuyesa angel Michael akuti "no"
Kuyesera king Davide akut "no way"
Ngat uli ochimwa palibe njira ina
Tsiku lomaliza kumwambako usakalowe
Haah
Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Lapilatuu
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Nyengo yovuta koma osakhulupilira
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Koma jah jah sazakukhulupilira
Akufa adzauka, Kaya osauka
Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
Tidzaona misonzi
Panzerepo limodzi
Iwe
Amakupatsa chilichonse chomwe umafuna
Nanga bwanj ulemu osampatsa
Ndizija amakulanda chilichonse, akaona akakupatsa iwe umatasa
Ndeno ma man mutha kulapa kuyisintha nkhani
Satana mdani, ukapusa akuika pa mpani
Azaliza lipenga
Tsiku lomwe lokha mphwanga palibe kuzemba
Azaliza lipenga
Alibe nazo ntchito zoti iwe umafalitsa uthenga
Kaya iwe uma trender
Kaya doctor umachiritsa matenda
Kaya fans ikakuona imapanga
Tsiku lomaliza ndila namalenga
Tsiku lobwera yesu
Lipenga lidzalira ngat ukuchimwa lapilatu
Lapilatuu
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Nyengo yovuta koma osakhulupilira
Kudzakhala kulira, kudzakhala kulira
Koma jah jah sazakukhulupilira
Akufa adzauka, Kaya osauka
Kaya wachithumba Kaya unali otchuka
Tidzaona misonzi
Panzerepo limodzi

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители