I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu) I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu) Ambuye (Ambuye) Ambuye (Ambuye) Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye) Ambuye (Ambuye) Ambuye (Ambuye), Ndikuthokoza Ambuye Eeh eh eh Iyi ndi nyimbo yafuko langa, my daily worship Ndikuvutika simunandisiye chonchi Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot Nde kulikose ndingapiteko tili limodzi Abale ndi alongo zikavuta amathawa Mavuto, pa mtendele simumansintha ma colour Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande Poti masiku sakoma onse, ndi nthawi chabe Iyi ndi daily worship, nyimbo yafuko langa Kenako ukamvera uzipezamo ka bata Osamathamangila kunena kuti sanayankhe Chifukwa olo mpweya tikupumau ndi wake Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa brazi Mufuna mudwale kaye kuti muyamikire nthanzi Wina amwalire kuti muyamikire moyo Akachedwa kuyankha mumasiya kukhala loyal Ndeno Tate wanga ndufuna kukhala munthu wa humble Poti ndikuziwa mumapasa, mumalanda Komanso ndukufuna ndikhale chitsanzo Mfana wa mature poti chibwana chimalanda Kuchepesa anga, bible likhale mzanga Munthu kundiyamba ine kukhululuka nsanga Kupewa ma blanda, Jajah mu mtima mwanga Tsiku lomalidza kuchongetsa dzina langa Ambuye (yea yea yea yea) Ambuye (yea yea yea yea) Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye) Ambuye (yea yea yea yea) Ambuye (yea yea yea yea) Ndikuthokoza Ambuye (Ambuye eeh) Uuh uh uuh I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu) I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu) Ambuye Ambuye (no one like you) Ndikuthokoza Ambuye (Yesu) Ambuye Ambuye (no one like you) Ndikuthokoza Ambuye (Yesu) Uuh yeah yeah Uuh yeah yeah