Kishore Kumar Hits

Sean Morgan - Ndidzagenda текст песни

Исполнитель: Sean Morgan

альбом: Ndidzagenda


It a sign of a big league yeah
Aaah aah
Run it
Eya big man Sean
Luso lanu ndilochititsa kaso
Mumayimba dancehall ina-ina dancehall
Mumapinda beat nokha kuwongoletsanso
Mundimvetse musazitaye izizi
Ngati ndafika pokuwuzani izizi
Tafika potopa nazo izizi
Pamawa musadzati sinanene izizi
Zomatulutsa tune kukhala chinthawi
Mumafuna ghetto idzimvera chani?
Mu ghetto mumangotipatsa zinkhani
Zinkhani zinkhani adha aja ndichani?
Mukadzangoti zii kwanu ndidzabwera
Inde ndidzafika kwanu ine ndidzagenda
Ndidzakhala ndakwiya ndi ma temper
Ghetto ikhala bwanji simukuyimba?
Aah please chonde
Ndikakwiya simungandikonde
Mudzapha gulu
Luso limalimbikitsa gulu
Mesa munali ku MUST Ndata
Eya mwamaliza ku Ndata
Sizoti mukhale pansi kwacha
Anzanu akutulusa ma hit song mwamva
Nyimbo zanu zinatichotsa kutali
Tilowere kuti pakati olo mbali?
Mwatisiya tokhatokha kutali
Kutali kutali kutali kutali
Zomatulusa tune kukhala chinthawi
Mumafuna ife tizimvera chani?
Mu ghetto mumangotipasa zinkhani
Zinkhani zinkhani
Kodi adha aja ndichani?
Mukadzangoti zii kwanu ndidzabwera
Inde ndidzafika kwanu ine ndidzagenda
Ndidzakhala ndakwiya ndi ma temper
Ghetto ikhala bwanji simukuyimba?
Aah please chonde
Ndikakwiya simungandikonde
Mudzapha gulu
Luso limalimbikitsa gulu
Mesa munali MUST Dada?
Eya tamva mwamaliza ku Ndata
Sizoti mukhale pansi kwacha
Anzanu akutulusa ma hit song mwamva
Mukadzangoti zii kwanu ndidzabwera
Inde ndidzafika kwanu ine ndidzagenda
Ndidzakhala ndakwiya ndi ma temper
Ghetto ikhala bwanji simukuyimba?
Aah please chonde
Ndikakwiya simungandikonde
Mudzapha gulu
Luso limalimbikitsa gulu

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители