Kishore Kumar Hits

Xenoo - w górę w dół текст песни

Исполнитель: Xenoo

альбом: w górę w dół


Mmmmmmmmm
Simple son
Kulibe maso
Kulibe maso
Anzanu ajah
Anali pompa
Achimwene ajah
Anali pompa
Achemwali anu ajah
Anali pompa
Amakunenani amakunenani
Akt mumazifila NGATI gettoh
Yonse mumaimilira
Ati mukangovala ka fila
Pachulupo mumaima
Ati inuyo mumazimva
Ati inuyo mumazimva
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Koma yesu amaziwa
Koma yesu amaziw
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Koma yesu amaziwa
Koma yesu amaziwa
Olo akunene akujede amvekere
Ndiwe wasatanik
Olo akujede akunene amvekere ndiwe wanyanga
Km Mulungu wako ndiwamoyo
Km Mulungu wako ndiwopuma
Azakupulumusa
Kumisampha yaoipayo
Poti sungaziwe zomwe anena
Km yesu amaziwa
Km poti sungaziwe zakumbuyo
Km yesu amaziwa
Azakupulumusa kumisampha ya Satana
Azakuimbosa kuzoipa zasatanayo
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Koma yesu amaziwa
Koma yesu amaziwa
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Koma poti kulibe maso
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Sungaziwe zakumbuyo
Kumbuyo
Koma yesu amaziwa
Koma yesu amaziwa

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Jvnek

Исполнитель

hichi

Исполнитель

Mejbi

Исполнитель

nomy

Исполнитель

ERES

Исполнитель

K.M.S

Исполнитель

DaNON

Исполнитель

MtZ

Исполнитель

PEGE

Исполнитель

Zuyeh

Исполнитель