Kishore Kumar Hits

Onesimus - Allegik текст песни

Исполнитель: Onesimus

альбом: Allegik


Butter
It's butter baby yah
Ah huh
Allegik, Allegik, Allegik
Allegik, Allegik, Allegik
Ukatalikila ndi mavutika ineyo
Ukangosutha ndi mabanika, ah
Mutu sumagwila, mutu sumakoka
Zoti ndi dealer pa town zosamveka
Mutu sumagwila, Mutu samakoka
Zoti Ndi Doba pa town zosamveka
Ngati Ali juju munanditha baby
G-Sali stable pano ndi teke teke
Gelo asachoke ineyo gwede gwede
Pitikoti government, mpheche peche
Ngati Ali juju munanditha baby
G-Sali stable pano ndi teke teke
Gelo asachoke ineyo gwede gwede
Pitikoti government, mpheche peche
Allegik, Allegik, Allegik, yah
Allegik, Allegik, Allegik, yah
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Allegik, Allegik, Allegik, yah
Allegik, Allegik, Allegik, yah
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Ma group mu akuti ineyo ndapenga
Mental disorder yapa zombayi ndaposa
Ndili busy ine ndi vama love
Azinzanga samabwela kwanthu
I don't know what you did to me
Mami don't stop me coz I like it
I don't know what you giving me
Ipatse moto Mamie coz I want it
Ngati Ali juju munanditha baby
G-Sali stable pano ndi teke teke
Gelo Asa choke ineyo gwede gwede
Pitikoti government, mpheche peche
Ngati Ali juju munanditha baby
G-Sali stable pano ndi teke teke
Gelo asachoke ineyo gwede gwede
Pitikoti government, mpheche peche
Allegik, Allegik, Allegik, yah
I'm Allegik welewoh
Allegik, Allegik, Allegik, yah
I'm Allegik
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Allegik, Allegik, Allegik, yah
I'm Allegik welewoh
Allegik, Allegik, Allegik, yah
I'm Allegik
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Sindifuna wina komano Iweyo
Sindifuna pena, Komatu pa iweyo

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель