Kishore Kumar Hits

Kell Kay - My Wife текст песни

Исполнитель: Kell Kay

альбом: Love After 24


From today, today, today
Ndizimkonda mkazi wanga
Kuyambila lero lero
I will only love my wife
From today, today, today
Ndizimkonda mkazi wanga
Ndikonda yekhayo, Ndikonda uyu
Ndati I will only love my wife
Ndasiya zomagona kwina
Ndasiya kugula zinthu kwina
Ndasiya zoma njoyesta ena ine
Pomwe mkazi wanga aku vutika
Pepa sindizakuzunzanso
Pepa sindidzasamala wenanso
Kuyambila lero lero
I will only love my wife
From today, today, today
Ndizimkonda mkazi wanga
Ndikonda yekhayo, Ndikonda uyu
Ndati I will only love my wife
I'll never leave you again
No more tears no pain
I love you 10 pa 10 iwe
Sindikanfika apapa opanda iweyo
Bwenzi ndili munthu wa wamba opanda iweyo
Chisamaliro chako, chikondi chako
Chandipangitsa kusintha ineyo
Chisamaliro chako, kusakwiyakwiya kwako
Kwandipangitsa kukukonda iweyo
Kuyambila lero, lero
I will only love my wife
From today, today, today
Ndizimkonda mkazi wanga
Ndikonda yekhayo, Ndikonda uyu
Ndati I will only love my wife
From today sugar ndidzigula wakunokokha
From today zonse ndidzipanga ndiwe wekha
From today sindidzalola ana anga akanenso ine
From today, today, today

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель