Kishore Kumar Hits

Eli Njuchi - Zisunge текст песни

Исполнитель: Eli Njuchi

альбом: The Book of Z


Mmm zisunge, zisunge, zisunge
Sende, sendee, sendela, sendelaa
Patabadwa amuna angapo, ankafunabe mwana wa nkazi
Mapemphero opanda yakho ndine ndemwe nthumazi
Ndi ndi ndi ndiwe m'dalitso, Yankho ndiwe yankho
The day they brought you home kunagwa mvula
You are truly a miracle
Maso angawa, ndaona zinthu maso angawa
Imva ndamva zinthu makutu angawa
The world is not a safe place for you nde dekha bae umve
Zissuuuuunggeee
You have a beautiful name with a beautiful future, Yankho uzisunge
Zisuuuuunggeee
You have a beautiful name
You have a beautiful name
Zisunge
Zisunge
Zisuuuuunggeee
Zisunge
You have a beautiful name
You have a beautiful name
Zisunge
Sorry I wasn't home for your holiday
Sorry I wasn't there for the new year
Sorry for being a very busy brother, just like father
Busy climbing up the ladder
Mapemphero kumwamba, osayiwala Amen
Ndimakukonda you are so special, dollar yawo akhale wa commercial
Izakwana nthawi uzaziwa zosowa zako, uzazindikila mpavu ya ndalama
Abale anzathu sangapange afford zonse, ndiyankhula zonse
Izakwana nthawi yazinjoyi, nthawi yachikondi
You are gonna be blinded ndi anzako ochepa omwewo ena sazakhala mbali yako
Izakwana nthawi yosweka mtima, zinthu pena kuyenda, Pena kuyima
But anyways you have a bright future, sindizalola kuti uzatayike
I wanna see you fly high, Yolanda rule like a leader, J Banda
Sindizalola uzikumbile manda, nzeru zako Yankho uzimangile mpanda
Say no, know that you are priceless
Say no Thupi lako simalonda
Saay noo!! ndizakhumudwa ukazatayika Yankho
Zissuuuuunggeee
You have a beautiful name with a beautiful future, Yankho uzisunge
Zisuuuuunggeee
You have a beautiful name
You have a beautiful name
Zisunge
Zisunge
Zisuuuuunggeee
Zisunge
You have a beautiful name
You have a beautiful name
Zisunge
Zisunge
Zisunge
Zisunge
Zisunge

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Why

2021 · сингл

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель