Dzina Ndi dzina liti lingadzankhale Mwina ndima twins Wina wammuna Wina wamkazi Julie I've wrote a letter for you Mwina John, I've wrote a letter for you My love Hello my future daughter How is school? Ngat umakonda adad give him high five Hello my future son Geli ili bwanji? Ngati ndili pafupi, ubwele undihage Pakadali pano Sindidakumane ndi amai ako One thing I know She's a loving and a caring lady Za obvious, I am the funniest father Za obvious, I am the very best father Ukamandiona mu future Dziwa ndine hero Ngati ukumadya kugona Son be greatful 2022 mwanawe, its a tough time for your father Ma pressure ma pressure Mwana wamamuna ma pressure Ndikanali vendor, searching for your better life kumibawa Ndikanali lova, fighting for your better future ku limbe Ngati ndiike jump gear, fast forward Pena ngati ndingogiver ndikudina fast forward What easily comes easily goes my daughter Petience Ndili kubwela see you soon my son Confidence Dzina Ndi dzina liti lingazamukhale Eti sispence? Dzina Ndi dzina liti lingadzankhale Am gonna watch you grow Until you grow old Round of applause On your wedding and gala