Monga mwana wang'ono amadalila kholo Kutsala yekha amakanitsitsa toto Saayenda yekha angakagwele kumphopho Kusangalatsa namalengaso ndi choncho Osati matukutuku Ngati ukukankha chikuku Pamaso pamunthu wankulu Osadutsa mukusuta ndudu Chisomo chake ndichokwanila tonsefe Chitsanzo ndi mwana wa Maria ndi yosefe Pofunika mtanda wake tiwusenze Chomwechi mpakana kumalembe Poti iye ndi syllabus Timulonde mapazi Tisachite manyazi Akationa nkumati Mwana uyu uyu uyu Mwana uyu uyu uyu Ndiwanga aaa Ndiwanga aaaa Mwana uyu uyu uyu Mwana uyu uyu uyu Ndiwanga aaa Ndiwanga aaaa Ndifuna akandiona ine A-zi-ti Mwanayu ngwanga ine Nde chitsanzo ndi nsembe You'd think that he's a lannister The way he paid my debt!! Nde chili kwaine kufalitsa Eeehe Zachozizwa chomwe wachita Eeehe Nde kulikonse komwe nzapita I'll represent CHRIST to the fullest wazizur? Yeah Ambuye anati mfana wopanda ntchito you need some company Mu Aiguputo si Mo Salah upite Canaan Ndipo, ankadziwa ndani mwala okanidwa uzaBuilder mfana ankakugendani Posamila panga Chitsime cha kuya koma posamila phwanga Okontrola madzi mpaka osamila nkhwangwa Kusintha mfana wa magazi othamanga kuposa MiRa mpaka Timakuwa Abba Father Amandipasa ma khatcha ndikayamba kudya machaka Love yake jenuwini yosadyesana chi Banzi Ine chimwemwe kutsaya nthawi zonse akamati Mwana uyu uyu uyu Mwana uyu uyu uyu Ndiwanga aaa Ndiwanga aaaa Mwana uyu uyu uyu Mwana uyu uyu uyu Ndiwanga aaa Ndiwanga aaaa