Kishore Kumar Hits

Kelvin Sings - Aye текст песни

Исполнитель: Kelvin Sings

альбом: After The Honesty


Yeah...
Alright
Ndidzala mawu anu pakamwa pangapa
Nditama inu pakusuntha kwa lilaka
Manjenje ayi paliponsepo ndiponda
Ndiwope ndani poti ndinu ngaka yanga
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Ayi mpaka dzuwa litalowa
Everybody knows
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Ayi mpaka dzuwa litalowa
Chisomo chanu chandizungulira
Oyiwalidwa mwamukumbukira
Zomwe mumanena ndikhulupilira
Ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa
Ife tingoti
Amen Aye Amen Aye
Malonjezo anu
Amen Aye Amen Aye
Mukwaniritsa
Amen Aye Amen Aye
All your promises are
Amen Aye Amen Aye
Aye Aye Aye Aye
All your promises are
Aye Aye Aye Aye
All your promises are
Ndikhulupira chilichonse mumakamba
Pazinkhanira mudzayala gome langa
Oh when you say it is well
You never retract
Mumalizitsa ntchito yomwe mumayamba
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Mpaka dzuwa litalowa
Everybody knows
Baba you supply
Zonse zomwe ndimasowa
Kuyesa kufotokoza
Ayi mpaka dzuwa litalowa
Chisomo chanu chandizungulira
Oyiwalidwa mwamukumbukira inu Baba
Zomwe mumanena ndikhulupilira
Ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa
Ife tingoti
Amen Aye Amen Aye
Malonjezo anu
Amen Aye Amen Aye
Mukwaniritsa
Amen Aye Amen Aye
All your promises are
Amen Aye Amen Aye
Aye Aye Aye Aye
All your promises are
Aye Aye Aye Aye
All your promises are
Amen Aye Amen Aye
All your promises are
Aye Aye Aye Aye

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Aye

2021 · сингл

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель