I think ndiluda Ndidzachita kuyikira ngati chi ujeni Alright, keys Mmh ah, mmh uh Kunja kwacha, mavuto ndi omwewa koma tsiku langosintha Mdima wagwa, nyimbo ndi yomweyi koma oyimbva wangosintha yeah Mtima wanga unasweka kale Pena ndiyesa ngati ndilibe m'mbale Kusowa woti angandithangate, (ey yeah yeah yeah) Tsogolo luwoneka lopuwala, komabe ndiyimba Mwina mavuto nkuzilala Misozi ikamanga nyumba pa masaya Comfort me, zitoliro ndi gitala Mkakhala chete, m'makutu mwanga mumaveka nyimbo For sometime mtimawu supweteka Chowawa chimagwera mkati Mayesero a moyo wanga, (nyimbo ndi likasa) Nkhawa ine nkhawa ine, (nyimbo ikatha) Eeh nyimbo ikatha, (ndiyimbe) Nyimbo ikatha. (ndiyimbebe) 'Cause as it plays i'm alright I'm alright, i'm alright Maloto anga ndimalota ndili ntchana Anthu ambiri dzina langa akuliyitana Mayi angosekelera akandiyang'ana, (yey yeah yeah) But later on own reality strike and i'm Back with me fellas, chillin' on the block and The sun ah rise and ah set we ah watch it We pray fi di blessings and we grind till we haffit but, (poo poo poo) Whom Jah Jah bless though No man can curse now Blage Yala strum, ikanso drum Tiyimbe nkhawa tipachike Poti tikhakhala chete M'makutu mwanga mumaveka nyimbo For sometime mtimawu supweteka Chowawa chimagwera mkati Mayesero a moyo wanga, (nyimbo ndi likasa) Nkhawa ine nkhawa ine, (nyimbo ikatha) Eeh nyimbo ikatha, (ndiyimbe) Nyimbo ikatha. (ndiyimbebe) 'Cause as it plays i'm alright I'm alright, i'm alright ♪ Ey, hey yeah Mayesero a moyo wanga, (nyimbo ndi likasa) Nkhawa ine nkhawa ine, (nyimbo ikatha) Eeh nyimbo ikatha, (ndiyimbe) Nyimbo ikatha. (ndiyimbebe) 'Cause as it plays i'm alright I'm alright, i'm alright Mayesero a moyo wanga, (nyimbo ndi likasa) Nkhawa ine nkhawa ine, (nyimbo ikatha) Eeh nyimbo ikatha, (ndiyimbe) Nyimbo ikatha. (ndiyimbebe) 'Cause as it plays i'm alright I'm alright, i'm alright Yeah