Yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona, gona
Kunkonda pogona
Amandifuna pogona, gona
Kunfuna pogona
Kumbali amandikana, Amati ine ndine hule
Kumbali amandiyoza, ati ndine osauka
Kumbali amandikana, amangoti ndine nzake
Kumbali amandiyoza, ati ndimankakamila
Koma zikamuvuta amabwera Kwathu, baby ine ndakusowa
Koma zikamuvuta amabwera Kwathu, baby ndili nawe nkhani
Komatu sakamba ayi, amangokhala pa easy
Komatu sa-talker ayi, timangodziwa ma PG
Ndimalakalaka nditabweza chipongwe Koma ine zimandikanika
Ndimalakalaka nditabweza choyipa koma ine zimandikanika
Ndimamukonda ine, sindifuna atandisiya
Ndimamufila ine, sindifuna ntamusiya
Komabe, amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona, gona
Kunkonda pogona
Amandifuna pogona, gona
Kunfuna pogona
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah, prr
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя