Yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
Palowa njoka pano ndiye mkundifunano
Dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
Dzana dzanali munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka
Amakufuna zikakhalatu zawavuta (yah, yah, yah, yah)
Yah, amakufuna zikakhalatu zawathina (yah)
Yah, koma ku party umva asabwere amene aja ndachamba (yah)
Koma ku ukwati umva asabwere amene aja ndamowa (Oh, my God)
Yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano
Palowa njoka pano ndiye mkundifunano
Dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu
Dzana dzanali munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka
Yah, amafuna uzivutika
Amafuna uzingopempha
Amafuna uzisawuka
Inenso ndekha ndisamapushe, yah, yah
Pano panalowa njoka
Ka banja kajaso kanatha, panalowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka (palowa njoka)
Palowa njoka
Yah, yah, yah, yah, yah
Yah, yah, yah, yah, yah
Panopa panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panopa panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panalowa njoka (panalowa njoka)
Panopa panalowa njoka, rr
Yah, yachina Seven adah
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя