Blessings after blessings
Blessings after blessings
Yeeah yeaah
Yeahh yeeahh
Yeaah yeah
Mmmhhhhh
Yeeh yyeh
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Ndimakuona iwe ndiolimbikila
Ulibe maphokoso ndi anthu ndiwa mtenderele
Umaoneka smart chokhacho ummasangalatsa
Umaganiza smart chokhacho chimandiwaza
Ndimakuona iwe ndiwachilungamo
Umathandiza azako ngakhare tiri tochepa
Ulibeso tsakho macheza tonse ndaamozi
Ulibe chipako popeza tonse ndaamozi
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Iwe taima kaye, mmh
Anthu amakukonda, mmh
Ice taima kaye
Uli ndi mwayi mmh
Iwe taima kaye mmh
Wandisangalatsa mmh
Iwe taima kaye mmh
Utha ukhala Mlungu
Mmmmmmhh alipo enaso ndaazako omwe samakuonera bwino
Koma mmatope ovutika vutika tika kuolokamo
Ambiriso akuvutika kufunitsitsa utagwera momo
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Moyo wako uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwino
Uzakhala bwinoo
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя