Yeh yeh Yeaah yeaah Yeh yeh yeh yeh yeah Yeaah yeaah Ife ndi Mafana oti basi Ndukuuzani arasi Zofuna zathu sizambiri Mufuna chani? Malawi gin basi Ukafuna ukatipeza ku show Pakhomo zingati? Five pin basi Carina ya m'dala tasiya pa mbowee Abraz tikwera minibus Ife ndi Mafana oti basi Ndukuuzani arasi Zofuna zathu sizambiri Mufuna chani? Malawi gin basi Ukafuna ukatipeza ku show Pakhomo zingati? Five pin basi Ife ndimafana oti ah huh Ife ndimafana oti basi Akafunsa wakutuma ndi Malinga Nyama kuseli tikuzinga You is a Vegan eko zikapinga Me juss dribble inna di middle Camavinga mmmh Mafana bwanji mufuna kumandipinga Kundiyenda ngati njoka mukapinga Mu njale mwanga mwangodzadza dzima singer Ukafuna cross crew yonse ndima winger ah huh Ife ndi Mafana oti basi Ndukuuzani arasi Zofuna zathu sizambiri Mufuna chani? Malawi gin basi Ukafuna ukatipeza ku show Pakhomo zingati? Five pin basi Ife ndimafana oti ah huh Ife ndimafana oti basi Zima bouncer kuseli kudya bench Mkazi wa malonda timukhomela bench Sober man lero nde akhuta quench Bar man ndamuuza keep change Martse ananena kale loud and clear Kupatula mkazi wanga chomwe ndimakonda ndi beer Kuyenda ndi ma tradi kumwela kwa TA Amene takonzeka tiyeni King size Lizzla ndiyemwe ndikusut'la Zima mamie kufupi zungosunth'la Ma style ndungosintha kamas'tla Pa counter ma shot tungoshu'tla Ife ndi Mafana oti basi Ndukuuzani arasi Zofuna zathu ndizambiri ngati? Njee Malawi gin basi Mu kafuna mukatipeza ku show Pakhomo zingati? Five pin basi Ife ndimafana oti... ah huh Ife ndimafana oti basi Ife ndi Mafana oti basi Ndukuuzani arasi Zofuna zathu sizambiri Mufuna chani? Malawi gin basi Ukafuna ukatipeza ku show Pakhomo zingati? Five pin basi Ife ndimafana oti... ah huh Ife ndimafana oti basi