Kishore Kumar Hits

Crispy Malawi - Ukununkhila текст песни

Исполнитель: Crispy Malawi

альбом: MLW Tape1


How many Times Should I tell You? Kuti ndimakufila
Ndikungofuna Tizi Tchira
Ukudripa ndikumila
Fe fe fe fe UKununkhila
Ma Guy mwandilira
Ngati Mmaona Chithako chi muzachigwira
Pa corner ndakupanilira
Mmh ndakumatilira
Sindiku tripa kuyankha Text phone yangothima
Bend Down Ngati Ukulima
Kuthoka za Chilima
Ine ndikulima
Mmmh mmh don't holla Please!
Ndili High ndadya Cannabis
Ati Spe What is This?
Ukugwira Ass koma ufuna Kiss?
Hit n Run i never Miss
Ndikablowa imakhala Kiss
Eeeh ndimakhala Busy
Nde USAndipase Busy
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakuFila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fe fe fe fe UKunukhila
Fe Fe Fe Fe Ukununkhila
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakuFila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fe fe fe fe UKunukhila
Fe Fe Fe Fe Ukununkhila
Uli fly sukufunika Visa
Life is Too Short ngati Teaser
Ndili busy Minding my Business
Makape Ali mmadzi tikuwabatiza
We in The Cut ngati ndi Scissors
Wavala Bum short ndima Lipha
Ndango Rocker Zima Yeezus
Tili Mangochi walking on Water
Ndikungozifila Ngati Jesus Splash!
Shes better Than my Ex
Chi Body Cha Bho
Tipange invest
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakufila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fefefefe UKunukhila
FefeFefe Ukununkhila
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakuFila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fe fe fe fe UKunukhila
FeFeFeFe Ukununkhila
Yo Ndikuuze kangati? Kutindimakufila
Sindinakuuze dzina Chifukwa umandidziwa
Kaya uli ndi mamuna ndikungofuna kugwira
Zoti sukufuna sindikufuna Kudziwa
Tivaye pa Awiri bwanji? Panotu pali phokoso
Kuvaya pafupi kangonunkhila ka Mafioso(Fe Fe!)
Kuvaya ku date moti kazidya Busy ma photo
Zonse ndi chabe man bola kugwidwa ndi dolo
Ndikuuze kangati?
Kodi iwe Jahmeera? Tikukufuna ndi angati?
Ndikungofuna Kudziwa
Undimvetse ndikamati
Hayze akungotchira
Unakandifunsa ine ndikanati
Ndakumangilira
Ndikumasula Asavutike kumayankhula
Ndikuziwa ali ndi Freed
Mfana Ophusha
Mnamuziwa kale kale Akumwa Shooter
USAkhale Ngati sukufuna Mfana Ophula
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakuFila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fe fe fe fe UKunukhila
Fe Fe Fe Fe Ukununkhila
Ndikuuze Kangati?
Kuti ndimakuFila
Ndikungofuna TiziTchila
Uku Dripa ndiku Mila
Fe fe fe fe UKunukhila
Fe fe fe fe. Ukununkhila

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

RNB

2023 · альбом

Похожие исполнители

Dali

Исполнитель

Toast

Исполнитель