Kishore Kumar Hits

Slapdee - Dzuwa текст песни

Исполнитель: Slapdee

альбом: Dzuwa


XYZ Entertainment
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi zduwa
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi zduwu
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Takana ku biliever ndise tili naminyama
Navenso venzo nveka munshe vinaleka naku wama
Tinalakwila ndani mutikambileko sorry
Mayeso yatikonka Bad izibika story
First yenze cholera, kwabwela loadsheding
Before nama corona tenze busy nama gassing
Tayambo payana teka teka its so disgusting
Nama busa balema navo vama fasting
Ku hood kwanga ba guy bafuna che ka certain
Bavale che pamala naka nsima ndiye curtain
Sibafuna navambili umoyo che ni dalisoul
Ambuye abwezepo nga muchila wamalinso
How did we get here nalema kuzifunsa
Kapena niu dalo(dull) sinasilize pa UNZA
Agogo ananiuza uzakula mwana chipuba
Vikaku vuta langa kumwamba upempe zduwa
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, Ambuye tidaliseni ndi zduwa
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Eh
Nauka mutu uzinguluka monga nenze pakampelwa
Pa FB tayali akali kumenyana na mwelwa
Could it be that I'm stressing or making a big fuss
I know that there's somebody looking for a face mask
Coz they die without a proper doctor or a nurse
Without the medication they will end up in a hearse
Are we, born with a gift or maybe blessed with a curse
With the afterlife I'm certain we might end up in a church
Just not longa ago nenzo nvelela seer 1
Enze once a topic patu napa bondi panu
Since when chinfine chinankalapo big issue
Sambani kumanja sanitize nama tissue
Now all my shows cancelled I'm living off my investments
Pray to God he save my family and my best friends
Everything quarantined house, money, Car
Pray for zambia, for the globe for africa
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa,
Ambuye tidaliseni ndi zduwa
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Dzuwa, Ambuye chosani dzuwa
Dziko la ngenewa nguwe
Ta zunzika kopanda dzuwa
Ooh oo dzuwa, ambuye tidaliseni ndi zduwa
Zdiko ziko lichita nga yangenewa dululu
Tiyamika Mweo Apo pampando
Dzuwa dzuwa dzuwa

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Dizmo

Исполнитель

Jemax

Исполнитель

T-Low

Исполнитель