Ambuye, Ambuye Mulungu
Ine ndikudandaula usiku ndi masana
♪
Ambuye, Ambuye Mulungu
Ine ndikudandaula usiku ndi masana
♪
Ndili kulira, mayo, mayo
Ndili kulira, kulilira maso
Ndili kulira, mayo, mayo
Ndili kulira, kulilira maso
♪
Ndinali kuyang'anira mphatso kuchoka kwa Mulengi
Tsopano ndatopa, ndiponso ndakalamba
♪
Ndinali kuyang'anira mphatso kuchoka kwa Mulengi
Tsopano ndatopa, ndiponso ndakalamba
♪
Kodi ndi chiyani kumvetsa chifundo
Told you kupemphera
Kodi ndi chiyani kumvetsa chifundo
Told you kupemphera
Patse, patse ndi kulanda
Munanena mbuye
Mwana wa ufulu
Apatsa yekha
Patse, patse ndi kulanda
Munanena mbuye
Mwana wa ufulu
Apatsa yekha
Ndili ndi madandaulo
Mu mtima mwanga
Abambo anga, ndipuputeni misozi
Ndili ndi madandaulo
Mu mtima mwanga
Abambo anga, ndipuputeni misozi
Ndili ndi madandaulo
Mu mtima mwanga
Abambo anga, ndipuputeni misozi
Kulira sikuzatha iih, (ndili ndi madandaulo mu mtima mwanga)
Ah yeah, ah yeah kulira sikuzatha
Kulira sikuzatha iih, (ndili ndi madandaulo mu mtima mwanga)
Ah yeah, ah yeah kulira sikuzatha
Chimene ndinalakwa sindichiziwa
Zikundipweteka mu mtima mwanga
Ah yeah, ah yeah kulira sikuzatha
Chimene ndinalakwa sindichiziwa
Zikundipweteka mu mtima mwanga
Ah yeah, ah yeah kulira sikuzatha
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя