Zaka zambiri zatha
Iwe ine tikucheza
Mphekesera zimkamveka
Kuti ife ndichibwezi
Koma ife timkakana
Timvekere sizingatheke
Iwe ndi ine sitilola
Lelo ndatopa ndi mafunso
Omadzifunsa ndekha
Ine ndalema ndi mafunso
Ondifusanso wena
Chifukwa chomwe ndimadziwa
Mchoti ndimakukonda
Chimodzi chomwe mfuna mdziwe
Ndimve Pakamwa pako
Ngati umandikondadi ine
Umandifunadi ineeh
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Ndimafuna Ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Nthawi nde ikupita ah
Nthawi nde zikubwerabe
Chovuta kodi mchani
Kunena m'mene umamvera yeah
I need some assurance
Munthune ndikukula yeah
Nde tangonena
Tipange mapulani kodi
Zinthu zikhala bwanji
Poti ndatopa ndi mafunso
Omadzifunsa ndekha
Ine ndalema ndi mafunso
Ondifusanso wena
Chifukwa chomwe ndimadziwa
Iwe ndamene ndimakonda
Chimodzi chomwe mfuna mdziwe
Ndimve pakamwa pako
Kodi umandikondadi iwe
Umandifunadi iwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Ooh umandikondadi iwe
Umandikondadi iwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe
Ndidziwe
Mpatseko assurance
Munthune ndikukula
Mpatseko assurance
Munthune ndikukula
Mpatseko assurance
Munthune ndikukula ah
Поcмотреть все песни артиста
Другие альбомы исполнителя