Iwe ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Ka piece kokha, ka mtima wako Tandibenthulile chikondi chako Ka shoti kokha, undipatseko Unlock your soul, ndikukondeko Ka piece kokha, dilawitseko Ndimve kukoma kwa love yako Ka shoti kokha, ndisipeko M'maganizo mwako ndikhalemo Ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Iwe ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Baby ndibenthulile Ka piece ka mtima wako Ndibenthulile Ndibenthulile Ndibenthulile, ka piece ka mtima wako Ndibenthulile Check Pomwe ulipotu ndili pompo Ngati ungayende ndili konko Akazi ndi ambili koma mlingo wako ndwina Ngati nkhani ili level uli topo Enawatu kodi ndi mafuwa Koma iwetu wabuka moto Ka ganja timapoto Koma osamakayika baby girl Sikutitu ndine smoko Ka piece kokha, ka mtima wako Tandibenthulile chikondi chako Ka shoti kokha, undipatseko Unlock your soul, ndikukondeko Ka piece kokha, dilawitseko Ndimve kukoma kwa love yako Ka shoti kokha, ndisipeko M'maganizo mwako ndikhalemo Ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Iwe ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Baby ndibenthulile Ka piece ka mtima wako Ndibenthulile Ndibenthulile Ndibenthulile, ka piece ka mtima wako Ndibenthulile Kali kokha ndikanyama Titha kumakhalana Yenda limodzi osasalana Kuyenda manja titagwirana Mtima wako anakuswela Izo ndidzapadzana Tidzinthuto nditolela mama Kamudzi kakhala kanga aka Ndipo kasamalila Misonzi kusiya kulila Kusowa ponamizila Hold you tight kukazila Osachedwa ndikuganizila Osatalikila, tayandikila Zonsezi tamavetsela Ndingofuna utandibenthulila Ka piece kokha, ka mtima wako Tandibenthulile chikondi chako Ka shoti kokha, undipatseko Unlock your soul, ndikukondeko Ka piece kokha, dilawitseko Ndimve kukoma kwa love yako Ka shoti kokha, ndisipeko M'maganizo mwako ndikhalemo Ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Iwe ndibenthulileko Ka piece ka mtima wako Baby ndibenthulile Ka piece ka mtima wako Ndibenthulile Ndibenthulile Ndibenthulile, ka piece ka mtima wako Ndibenthulile