Kishore Kumar Hits

Baxxy Mw - Itanani Alonda текст песни

Исполнитель: Baxxy Mw

альбом: Pray, Hustle & Vibe


Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Fresh out the shower goddamnit I look too clean
Link up with the gang umadziwa ya ma 2 pin
Straight shots ndi mandimu five boys 2 gin
Mmene ukuthera mowa nza matsenga ngati Houdini
Moto Buu
Beat guuu
Drip chuu
Really cool
Fine boys pick a boo
Kwayaka moto it's really true
Priddy Ugly situation yeah I'm in the Mood
ZimaJoker I'm picking two
Ndine Baxxy who is you
Itanani a G4S
Six pack siikwana, give me one more case
Osandipatsa pressure aise, I don't need no stress
Chonde osandiponda aise yeah I just need more space
Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Mmene zilili man nyambalo mani lololo
Kalikonse tikaona lololo
Walimba mtima kubweresa wakoyo
Zilombo lololo
Matchelanso nawo angozaza lololo
Zipyangu paliponse lololo
Ndipo lero kukhala zigogodo
Yanga ija pa mabotolo
Breaking bread with the team pa chi sosholo
Kutikita kalikonse, popha nyani saona nkhope
Mani uko fokolo
Wabwera wekha koma busy kumapempha
Ah ah, konko uko
Matokoso anuwo konko uko
Tima beef tanuto konko uko
I mean, Moto ngati Quest, moto wake wa Flames
Mdub footprinting all the steps
Moto paliponse, none of you of ohns can contest
Uno coming correct, like the enemy of the state
Serial killing these beats, and I'm so obsessed
Bwalo likulile Atchalo alowe
None of you clowns wanna mess with the vets
Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Kacheze ndi a size yako uko
Nthawi yathu tingotayitsanapo
Za mowa ndilibe tsankho
Mabotolowo nde abweleletu angapo
Si mmene ndabukila
Si mmene nzeru zakulila
Mukatopa kundilangiza muchila
Makape, musapeze potchukila
I came ready, osawonetsa mtima wofooka
Bad man settings, yatsani cha Nkhotakota kuchikoka
Ma bosso ngati BMG
Strictly business EPMD
Tiwuchapa nkhani ya stireti
Cut out the background like a PNG
I got mad love for these banknotes
I got wild thoughts for these wild thots
I got sex drive for the both of us
If you tryna come you can park yours
Pano pachitika ngozi
Pano madzi afika m'khosi
Can't get my number you should pass yours
Ndayaka sin'kupasilika cross
Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Itanani alonda, kuno kwachema
Kwayaka moto, ngati gahena
Chonde osandiponda, ona ndatchena
Ndayaka moto, ngati gahena
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi
Bwalo likule tchalosi
Tchalosi, tchalosi

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Dali

Исполнитель

Toast

Исполнитель