Kishore Kumar Hits

Baxxy Mw - Ndimakomedwa текст песни

Исполнитель: Baxxy Mw

альбом: Pray, Hustle & Vibe


Iweeeeeee
Osandiyitanira ndilibe dollar, ndimakomedwa
Osandiyitanira mukangocalla, ndimakomedwa
Osandiyitanira zistango, ndimakomedwa
Osandiyitanira zipyango, ndimakomedwa
Ouh Ndimakomedwa
Kuyamba ndi Kuche Kuche mmodzi mpaka m'ngalande
Kuyenda ndi khoma mwadzandi dzandi, mpaka ndagwa eeeh
Ndimati ndichilla 30 minutes yokha, mpaka kwacha mbee
Akundiyimbira kuti tichotse matsile, choncho ndingalape
I'd rather be at the crib homie
Ndimakomedwa, that is a true story
That ain't no cap my nigga if you know me
Sindichedwa kubhoyila ndili ngati Indomie
Kubwata ngati Indomie
Osandiyitanira ndilibe dollar, ndimakomedwa
Osandiyitanira mukangocalla, ndimakomedwa
Osandiyitanira zistango, ndimakomedwa
Osandiyitanira zipyango, ndimakomedwa
Ouh Ndimakomedwa
Kuno kwabwera mahushasha
Ine manja mmutu, shashasha
Then I pull up kuti tchatchatcha
Grab a beer, take a shot shot shot
Lero nde tiutoucha cha cha
Chi muvu, ndikunja nja nja
Too wavy, ngati nyanja nja
Kwayatsidwa zi ganja nja nja
Zinthu zikatele sizimatha bho
Ndimakomedwa, ndimatengeka ndi stango
Bhebhi kubuzza bhebhi kuyimba, osayimva call
Nnalibe dollar, koma ndayaka ndadya floor, mpakana ndadya floor
Osatiyitanira kuzima show ngati simuku-payer
Gig yokhayo sitikuplaya
Ndaachina Jeydak sitikubhleya
Tili mu ghetto tikudya deya
Inu mukubwera, uku mukugeya
Tryna exploit us, and that is not fair
Tryna exploit us, and that is not fair
Osandiyitanira ndilibe dollar, ndimakomedwa
Osandiyitanira mukangocalla, ndimakomedwa
Osandiyitanira zistango, ndimakomedwa
Osandiyitanira zipyango, ndimakomedwa
Ouh Ndimakomedwa

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Dali

Исполнитель

Toast

Исполнитель