Iweeeeeee!!! Remix!! Dare Devilz Devilz!!! Ndimapenga misala ndikasanja Ndimasintha move ndimanjanja Kusambira mubhawa ngati nyanja Mowa ugone mmimba ife tigona panja Ndili wavy, ndili nice, ndikunanala Zoti ndimma three sindikusamala Ndazitola ndazitcheza ndine bhayala Ndamuuza ndine one atandifunsa nambala Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Ife nde tikumva kukoma Kudzadzidwa ma spirit tikuborna Kukwera ma speaker ndimakoma Nnagotenga VISA ndikutchona Kupanga zau savage koma tikufeela aire Kumwa waulere chifukwa chomveka pa wailesi Sipping on Skulls and CrossBones like a pirate Ena muli pa zero ngati njale yopanda Mileage Easy mani nafenso tili pa zero Weekend iliyonse mutu suugona pa pillow Osatsika weight kudya nyama by the kilo Kumaliza mkunda ndikumadzimva u hero Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Ife nde tikumva kukoma Ati amwene Marcus atenga boma Ngati mmene chilili chikondi ndiyanga dona Ukafuna kucheza tiyeni pachi corner, izo ndizoona Ndayaka ngati dzuwa Moto wapamafuwa Ndayambano kukuwa Ngati ndili paguwa Zafikano pa huwa I don't care who you are Ndinatapa shuwa Nnagwira chiphadzuwa Mfana odzichepetsa ofeelidwa, Nankhumwa Nnakuuzani osaopa koma inu mwanyumwa Chabwino mkazi wanu sinnadye nnamumwa Ndinapha zimabeat zambiri pano ndapuma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Ife nde tikumva kukoma Tikumva kukoma Iwe kaya zako izo Kaya zako izo Iwe kaya zako izo Kaya zako izo