Sinnabwere kudzacheza Dollar yi ndimayichaser Lilongwe mpaka Luchenza Sindufuna nzipemphetsa Whatchu say to the money Whatchu say to the bag Whatchu say to the money Whatchu say to the cash Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser Sindichaser bhawa ndimachaser mbwindi I'm tryna KNQR it all like my name is Sindi (Nsungama) And you know I gotta deliver, so ndimafaka ziwindi Right now I'm skipping town ndikulowa Mchinji Mchinji Chasing the bag the dough the only time that I'm running Growing these money trees 'cause it's way way too sunny Laughing to the bank like this money too funny Kupanga dollar kupanga khesh mwamakani Maluzi kubalalitsa Umphawi kutukwanitsa Ndalama kusalalalitsa Kunenapa tsaya ngati manyitsa Mavuto kubalalitsa Ndalama kukanganitsa Komabe sitikufooka ma file wa tikuthamangitsa Ndungofuna mandede Maluzi akundimvetsa m'bebe Ndikukunga plan ukandiona phee Ngati siza ndalama phwanga khala phee Whatchu say to the money Whatchu say to the bag Whatchu say to the money Whatchu say to the cash Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser Za ndalama tili mkati ngati ceiling Ndalowa Tunduma kusintha kwacha funa ma Shilings Only here to make some dough so fuck your feelings Umayamba ndi khodo then you to stack a Billion Geni siimachepa braz, olo yama handede handede Changu ndungofuna cash, run it andele andele Ndipo mfana otidissa, kumvetsa m'bebe tsa m'bebe Ndalama sindimayimissa ngati wansembe wansembe Ndungofuna mandede Maluzi akundimvetsa m'bebe Ndikukunga plan ukandiona phee Ngati siza ndalamaaa phwanga khala phee Whatchu say to the money Whatchu say to the bag Whatchu say to the money Whatchu say to the cash Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser Kumazisaka Kumazisaka Kumazisaka Kumayichaser Kumayichaser Kumayichaser