Woaaah Ngakhale ndimachimwa inu mmandikondabe Ndimalimbikira kuti mwina zingatheke Kupusha ka hustle kuti mwina tingamveke Timveke, ena asatiseke Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera All praise to the most high Madalitso ngosayamba Ndimayamika kumwamba Munandipatsa chi mpamba Mpaka kupeza ndalama ya fees Geni yake yamasamba All I do is pray ay Sindilowetsapo nyanga I gotta unlock these new levels I gotta unlock these new levels We've been thinking outside the box Plottin' with my new circle Nde magazi, tidutseko Magazi tidutseko Look out for opportunity windows akatseka zitseko I take care of my biz 'Cause this life is too hard bro How I take care of my biz I go too hard bro I go in guns blazing Like I'm holding two riffles All this that I have I owe it to God bro Ngakhale ndimachimwa inu mmandikondabe Timalimbikira kuti mwina zingatheke Kupusha ka hustle kuti mwina tingamveke Timveke, ena asatiseke Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera Hustle ndi yako Kumayipemphelera Kumayichengetera Kumayipatsa moto Kumayipemelera