Mma! ukamayenda, yeah yeah Yeah, baby ukamayenda Ndikudziwa umwetulira Mutu Wanga sukugwira Ukamayenda Nkhawa zimasefukila Mwina akuwona wina, Ukamayenda Ndimafuna nditakuwuza Baby bwelera kunyumba Ndili ndi mantha ndikuluza mwina akukoka wina Ukamayenda, Ukamayenda, Ukamayenda ♪ (Ndikudziwa umwetulira, Ndikudziwa umwetu, Dziwa umwetu) (Ndikudziwa umwetulira) Mutu wanga umayima, ukamayenda Maganizo anga ndikamawatengela pa mtima Ukumasweka, ukamaseka eh Anthu onse kukuchewukila iwe, unakadekha Zikundipeta, zokukhulupila ndi kukukayikilaso sindikumvesa Koma no lie, ndili momo mpaka muyaya Kapena mwina unandidyetsa konda ine Zokusiya zokha nde mayaz Ukasuntha ndi ma catcha no flight Si za no strings these are all ties Ukamandikayikila uzingomva izi We might not be forever but we're for life Baby ukamayenda Ndikudziwa umwetulira Mutu Wanga sukugwira Ukamayenda Nkhawa zimasefukila Mwina akuwona wina, Ukamayenda Ndimafuna nditakuwuza Baby bwelela kunyumba Ndili ndi mantha ndikuluza mwina akukoka wina Ukamayenda, ukamayenda, Ukamayenda ♪ (Ndikudziwa umwetulira, Ndikudziwa umwetu, Dziwa umwetu) (Ndikudziwa umwetulira) Uli mwetu mwetu Running for your heart mtima befu befu Ndilipodi ndekha? Ndifusiletu Ngati zili choncho banja ndifusiletu Sizokana eyetu Ukupita kuti kunjaku ndi kwa mphepo Bwelela kunyumba ngati reversal Even on a high horse sindili stable eish Za ma makonda izi Pena ngati ubwile Panado five Zikati zikome nde more life Kenako zithimbe ngati umwele madzi Si zoona izi Koma no lie Zokusiya zokha nde mayaz Ukakayikila uzingomva izi We might not be forever but we're for life Ukamayenda, Ukamayenda, Ukamayenda (Ndikudziwa umwetulira, Ndikudziwa umwetu, Dziwa umwetu) (Ndikudziwa umwetulira) Ukamayenda, Ukamayenda, Ukamayenda ♪ (Ndikudziwa umwetulira, Ndikudziwa umwetu, Dziwa umwetu) (Ndikudziwa umwetulira) (No lie, No lie)